Wife Material Lyrics
Kukakhala kunjaku kwacha bho... Yeah yeah
Kukakhala kunjaku kwacha bho
Zachita kudzadzamo bobobo
Wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Ndinapeza chibhebhi anthu adziwe
Sindimachibisa sichapadziwe
Yemwe zikumuwawa adhiwe
Koma ichichi ndi changa chi Lindiwe
Sichingazakupatse mphindi iwe chimakhala chili ndi ine uzimva iwe
Vuto lake iweyo kuzimva iwe umangogwira akazi openga ma byzwe
Za ife ndi zokoma zothila curry
Sitimvetsana kuwawa tsabola wa kale
Uyuyu ndi wanga si temporary
Ndikanena kuti ndimugaya si mphale
Kutentha ngati Nali samalani abale
Akusungila sugar wonyambititsa mbale
Mkazi uyu ngoiwalitsa abale
Amakomedwetsa ngati anthu a Ndale
Very Good Very Good
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a m'video
Mami muli pure ngati ka viligo
Mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
Ichi ndi chi ndiwo koma si mpiru
Sindinachite kuchiba koma ndi chi dhilu
Ichi ndi chibhebhi chodzadza feel
Dzina lake ndinaliyika kale pa will
Chimandikumbutsa Maggie Mwaupighu
Mahope anga a ku Primary ku Mphungu
Tili mafana oyankhula chizungu
She had a chocolate skin ndimamufila khungu
Chibhebhi changachi chandipatsa khungu
Ndikayenda m'townimu sindiona buthu
Ndadwala Chikondi 10 pa 10
Chachita kundifika pe mpeni
Ndavomera Mami ndi malizeni
Sindipempha kuti Ambuye ndichilitseni
Izi si za gulu si za m'memo
Ineyo ndili momo m'menemo
Very Good Very Good
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a m'video
Mami muli pure ngati ka viligo
Mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
Gal you di wife material
I just wanna make you my wife ooh
Gal you di one in a million
This feeling for you I can't deny ooh
Iwe ndiwe Mkazi wooneka bho wooneka bho wooneka bho
Iwe ndiwe chi Mkazi chooneka chooneka bho chooneka bho
Iwe ndi Mkazi wofitha bho wofitha bho wofitha bho
Iwe ndi chi Mkazi chofitha bho chofitha bho chofitha bho
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a m'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
WATCH VIDEO
ABOUT THIS SONG
Release Year : 2021
Album : Wife Material (Single)
Added By : Farida
SEE ALSO
AUTHOR
PHYZIX
Malawi
Phyzix is a multi-award winning Malawian recording artist, record producer, marketer, banker and ent ...
YOU MAY ALSO LIKE