Level Ya Madolo Lyrics
Iyi ndi level ya madolo (level yama dolo)
Ife sitizasika na (sitizasika nawo)
Pamwamba pamatikhala (pamatikhala)
Sitiyimba nyimbo zopala
Coz ndife madolo Iyi ndi level ya madolo
Maflo anga ndiachamba ndinkona amawabanda
Pakati pauyo ndi uja malyric anga amawaba nda?
I’m di fada pama beat ndine kholo(Scrrr)
Sife size yanu iyi ndi level yama dolo
Ndimapanga zomwe hater aMazda ngati
Car Ndinavaya pomwe ndilipa simuzafika
I’m on a new level inu mukupanga zachikale
Zolimbana ndima hater zija ndi zachikale
Ife sitizasika na (sitizasika nawo)
Pamwamba pamatikhala (pamatikhala)
Sitiyimba nyimbo zopala
Coz ndife madolo Iyi ndi level ya madolo
Ndimangoseka mfana akadissa me
Funsa mughetto mwanu ndani amene asadziwa me
Kuzipopa nkochuluka level yanu nde ndi ayi
Kodi mukamandi dissa inu simukhala ndi mphwayi
Mukafuna kusintha level just think about time
Siungathe kundimvetsa zaine pano zili fine
Ine ndi magiclevel (level yamadolo)
Alipo ambili mughetto (ondipanga follow)
Mulibe mano siyani kukamba za beef
Ndimamva chisoni mukamalimbana ndiife
I’m too Buddie like network yaku
Zimbabwe Olo mutadula miyendo koma pamic ndizaimabe
Chimfana chopanda mantha zima diss sindiziopa
Ndimayimba zothyakuka sindiyimba ine zolopa
Ine ndimfana o heater simungandizizilise
Mupange ndiomweo simungandipepelese
Ife sitizasika na (sitizasika nawo)
Pamwamba pamatikhala (pamatikhala)
Sitiyimba nyimbo zopala
Coz ndife madolo Iyi ndi level ya madolo
WATCH VIDEO
ABOUT THIS SONG
Release Year : 2022
Album : Level Ya Madolo (Single)
Added By : Munashe Chiputula
SEE ALSO
AUTHOR
YOU MAY ALSO LIKE