Home Search Countries Albums

Cha Nyo

PHYZIX Feat. DAN LU

Cha Nyo Lyrics


Ye
Yakayakayo (It’s Only Entertainment)
DJ OK/ Uli nyo
(Phyzix) Ye
(Very Good Very Good) Shooodooo

Amakudabula sadziwa
Worth yako anthuwa Kukuliza daily kukhala ngati kape
Ndiwe chi mkazi cha nyo (Cha Nyo!) Sadziwa (Eh!)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo eeya
Akanaona patali sakanakuseweletsa
Kukongola ndi mtima omwe mwana wa Mayi
Ndiwe chi mkazi cha nyo (Cha Nyo!) Ye
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo eeeya! Ye

Ma hip ako ali nyo
Nkhope yako ili nyo
Smile yako ili nyo
Khalidwe lako lili nyo
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo nyo nyo nyo (Cha Nyo)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo Ye
Ma hip ako ali nyo
Nkhope yako ili nyo
Smile yako ili nyo (eh)
Khalidwe lako lili nyo
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo nyo nyo nyo (Cha Nyo)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo eeeya! Ye

Pa iweyo ndispender bandulo
Mkazi wowala sitimabisa ngati ndi kandulo
Mkazi wa changamu wa no tulo
Unachita kukongola mofunika mendulo
Ambiri akunena ndiwe wamngwiro
Ubwere mu moyo wanga uzatenge chionglero
Kuthamangitsa midima ndi pemphero
Kunditetezera momwe achitila Angelo
Ndinali wachibwana papichulo
Kukula unachita kundilizila wezulo
Pano madalitso nde ndi dabulo
Yemwe wapeza mkazi wapezadi chabwino
Pakati pa usiku ndiwe Namwino
Masana kuchengetana moyo ndikumva bwino
Ndachita kuika seda ya nyooo
Kuti mwina mwake ndikutengemooo

Ma hip ako ali nyo
Nkhope yako ili nyo
Smile yako ili nyo
Khalidwe lako lili nyo
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo nyo nyo nyo (Cha Nyo)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo Ye!
Ma hip ako ali nyo
Nkhope yako ili nyo
Smile yako ili nyo (eh)
Khalidwe lako lili nyo
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo nyo nyo nyo (Cha Nyo)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo eeeya! Ye

(Cha Nyo)
Chi Mkazi Cha Nyo! (Cha Nyo)
Mwanakazi I thought I was done
Coz love is crazy
Ndinafika poti sindimafunanso chibwenzi
There was nobody to love me they were lazy
Amene amazayesawo samafika hands (100)
Amathera mu ma 50 m’ma 60, osafika 80
You came with the difference

Ma hip ako ali nyo
Nkhope yako ili nyo
Smile yako ili nyo
Khalidwe lako lili nyo
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo nyo nyo nyo (Cha Nyo)
Ndiwe chi mkazi cha nyo nyo Ye

Enjoy Synced Lyrics With Our Mobile App

Download on Google PlayGet it on App Store

WATCH VIDEO

ABOUT THIS SONG


Release Year : 2022


Album : Cha Nyo (Single)


Copyright : © 2022 It's Only Entertainment (IOE)


Added By : Farida

SEE ALSO

AUTHOR

PHYZIX

Malawi

Phyzix is a multi-award winning Malawian recording artist, record producer, marketer, banker and ent ...

YOU MAY ALSO LIKE