Home Search Countries Albums

Panado

ONESIMUS

Panado Lyrics


Panado Panado yeah Mmm
Ma headache yeah Mmm eeh
Panado Panado mmm eeh

Amakonda miseche
Amakondwa munthu adzivutika
Zochitika ngati siopemphera
Daily daily busy ntopola
Kubaya ma damage
Kuupasa moyo wanga challenge
Machitidwe awo ngati Judas
Makhalidwe awo ngati njenjete eeh

Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditaphokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditaphokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka

Ndi nsanje apatseni
Panado Panado
Panado Panado
Amweko
Panado Panado
Panado Panado
Mutu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka, mtima wachigawega
Mutu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka, mtima wachigawega

Samafuna ndiyendere njale
Zikandiyendera amakoka chibale
Zikamandivuta andinyoza kumbali
Koma Mulungu andichita balance, I relax
Amamenya nkhondo nditakhala pansi
Adani anga onse alemba m’madzi
Samakondwa nane

Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditaphokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditaphokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka

Ndi nsanje apatseni
Panado Panado
Panado Panado
Amweko Panado Panado
 Panado Panado
Mutu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka mwina ndi nsanje
Kaduka, mtima wachigawega
Mutu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka, mtima wachigawega

Enjoy Synced Lyrics With Our Mobile App

Download on Google PlayGet it on App Store

WATCH VIDEO

ABOUT THIS SONG


Release Year : 2021


Album : Panado (Single)


Added By : Farida

SEE ALSO

AUTHOR

ONESIMUS

Malawi

Onesimus is an Award winning Artist, Afro-pop /Singer, Songwriter celebrated across the world. ...

YOU MAY ALSO LIKE