Home Search Countries Albums

Chisangalalo

KELL KAY

Chisangalalo Lyrics


I’ve been praying for you daughter
It was such a long journey
Kukuona chonchi ndi umboni
Anapililadi your mami
Everyday I hope to remind you that you’re beautiful
As you grow I will keep reminding you that the world is yours to take
I got a call from your mama
Akuti I think ineyo ndili ndi mwana
Nafunsa waziwa bwanji
Akuti ndaziyeza so I know
We were so excited chisangalalo, we were so excited

Because of you
Chisangalalo, lalo
Because of you
Chisangalalo, lalo
Chisangalalo, lalo

Octavia, I will always be there
You know that I swear
Come rain or sunshine for you I will care
Everyday I count blessing men am lucky
Thank you God boy and girl yeah am lucky
I will be watching your back
My job as your Dad
I will put a smile on your face baby never be sad
Uli ndi m’bale wako
Ndufuna azakhale nzako
Limodzi mudzangonjetsa
Mapili mudzagwetsa
Koma uziwe mulungu
Poti ndiye mfumu
Zikomo kumwamba, zikomo

Because of you
Chisangalalo, lalo
Because of you
Chisangalalo, lalo
Chisangalalo, lalo
Because of you
Chisangalalo
Because of you
Chisangalalo, lalo
Because of you
Because of you
Chisangalalo mtima mwanga
Chimwemwe mtima mwathu

Enjoy Synced Lyrics With Our Mobile App

Download on Google PlayGet it on App Store

WATCH VIDEO

ABOUT THIS SONG


Release Year : 2021


Album : Chisangalalo (Single)


Added By : Farida

SEE ALSO

AUTHOR

KELL KAY

Malawi

Kell kay is a musician from Malawi ...

YOU MAY ALSO LIKE