Home Search Countries Albums

Njala

GODDY ZAMBIA Feat. LANJI

Njala Lyrics


Ne nibakonda alume angu
Nao onikonda, ovutikila banja yasu
Kuti tisakafwe nanjala ah! Ah! Ah!
Mwepeza nchito kukalale
Pe mwenzoluta mwenzeti mukawele
Lomba papita masiku anyinji
Bana balila njala ne nibape chinji?

Njala njala njala ahh njala mukawele liti?
Njala njala ahh njala njala njala mukawele liti?

Kuno mai ndinabwelera zanchito koma zonse ziti kuno kulibetu nchito
Ndina dikhira kufikira zakudya ndinatengazo zinata panjila
Ndalama zinagwa twenty kwacha ndinasala nayo yo inata
Ndinkhatumiza koma ten kwacha ndiyo ndinkasala nayo
Ndizayetsetsa kukongola kwa anzangu
Basi ndikatero nditumiza osadanda ndimagobo ndikumenya kuno ndi anzanga
Zikakwana zokwerera ine ndizachika
Kufika kuchika kufika kuchika kwathu konko
Kufika kuchika konko
Ndizafika kuchika kufika kuchika kwathu konko kufika kuchika konko

Njala njala njala ahh njala mukawele liti?
Njala njala ahh njala njala njala mukawele liti?

Ana ali bwanji? Inu muli bwanji?
Agogo mukukhala nawo kodi muli bwanji ? Ehhh
Mukaone amake dalitso,kuli chomwe ndatumiza konko kuli mavuto
mukufa njala ana njala ati mbuto zakubzyala munadya chiwaya
Ehh ija nkongole anatengako sabina inu tandiuza sanalete sarafina?
Njala njala njala njala ndidziwa mukufa njala
Koma ndikubwera konko posachedwa.

Njala njala njala ahh njala mukawele liti?
Njala njala ahh njala njala njala mukawele liti?
Eh njala ahh njala mukawele liti?
Njala aah njala aah mukawele liti?

Ndizafika kuchika kufika kuchika kwathu konko
Kufika kuchika konko
(njala njala njala ah ah ah mukawele liti?)

Enjoy Synced Lyrics With Our Mobile App

Download on Google PlayGet it on App Store

WATCH VIDEO

ABOUT THIS SONG


Release Year : 2022


Album : Njala (Single)


Added By : Farida

SEE ALSO

AUTHOR

GODDY ZAMBIA

Zambia

Godfrey Lungu popularly known by his stage name as GODDY (Goddy Zambia) is a fast rising Afrobeats s ...

YOU MAY ALSO LIKE